March 29–April 4
NUMERI 15-16
Nyimbo Na. 101 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Samalani Kuti Musakhale Wonyada Ndi Wodzidalira”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Nu 15:32-35—Kodi tikuphunzira chiyani pa nkhani imeneyi? (w98 9/1 20 ¶1-2)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 15:1-16 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Ulendo Woyamba: Yesu—Mt 16:16. Muziimitsa nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali m’vidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)
Nkhani: (5 min.) w15 5/15 15 ¶5-6—Mutu: Kodi Kunyadira N’kosiyana Bwanji ndi Kunyada? (th phunziro 8)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Musamatsanzire Anthu Amene Ndi Osakhulupirika”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Musamatsanzire Anthu Osakhulupirika.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 127 ndi bokosi lakuti “Munda wa Magazi.”
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 16 ndi Pemphero