Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Samalani Kuti Musakhale Wonyada Ndi Wodzidalira

Samalani Kuti Musakhale Wonyada Ndi Wodzidalira

Kora anagalukira dongosolo la Yehova chifukwa anayamba kunyada ndi kudzidalira (Nu 16:1-3; w11 9/15 27 ¶12)

Kora anali Mlevi wolemekezeka ndipo anali kale ndi maudindo ambiri (Nu 16:8-10; w11 9/15 27 ¶11)

Maganizo olakwika a Kora anabweretsa mavuto aakulu (Nu 16:32, 35)

Tisalole kuti zimene takwanitsa kuchita m’gulu la Yehova zitichititse kuyamba kunyada komanso kudzidalira. Ngati takhala m’choonadi kwa nthawi yaitali komanso ngati tili ndi maudindo akuluakulu, m’pamene tiyeneranso kukhala odzichepetsa kwambiri.