Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amatsogolera Anthu Ake

Yehova Amatsogolera Anthu Ake

Yehova ankasankha kumene anthu ake ayenera kupita komanso nthawi yake (Nu 9:17, 18; it-1 398 ¶3)

Anthuwa ankafunika kumvera mwansanga zimene Yehova wasankha (Nu 9:21, 22; w11 4/15 4-5)

Yehova ankagwiritsa ntchito anthu opanda ungwiro kuti azimuimira popereka malangizo (Nu 10:5-8)

Tikamamvera amene akutitsogolera, timasonyeza kuti tikumvera Yehova.