April 18-24
1 SAMUELI 23-24
Nyimbo Na. 114 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tiziyembekezera Yehova Moleza Mtima”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Sa 23:16, 17—Kodi tingatsanzire bwanji chitsanzo cha Yonatani? (w17.11 27 ¶11)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 23:24–24:7 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zimene anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo (th phunziro 6)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni chimodzi mwa Zinthu Zophunzira. (th phunziro 13)
Nkhani: (5 min.) w19.03 23-24 ¶12-15—Mutu: Muzileza Mtima ndi Amene Mukuphunzira Nawo. (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Mavuto Onse Ali Ndi Tsiku Lothera”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Anthu Ogwirizana M’dziko Limene Anthu ake Sagwirizana.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 14 ndime 18-19, mfundo za m’Baibulo tsa. 196-199
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero