April 4-10
1 SAMUELI 20-22
Nyimbo Na. 90 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mungatani Kuti Mukhale Bwenzi Labwino?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Sa 21:12, 13—Kodi tingaphunzire chiyani pa zimene Davide anachitazi? (w05 3/15 24 ¶4)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 22:1-11 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Wobwereza: (2 min.) Chitani ulendo wobwereza kwa munthu amene anachita chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. (th phunziro 6)
Ulendo Wobwereza: (5 min.) Pambuyo pa nkhani ya Chikumbutso, yambani kukambirana ndi munthu amene munamuitana ndipo muyankhe funso limene wafunsa lokhudza mwambowu. (th phunziro 12)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 04 mfundo 3 (th phunziro 20)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kodi Mumacheza ndi Ndani pa Intaneti? (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzichita Zinthu Mosamala Mukamacheza ndi Anzanu pa Intaneti.
Tidzalandire Bwino Alendo: (5 min.) Nkhani yokambidwa ndi woyang’anira utumiki yochokera mu Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu ka March 2016. Fotokozani mmene ntchito yoitanira anthu ku Chikumbutso ikuyendera. Tchulani za ndandanda yowerengera Baibulo pa nyengo ya Chikumbutso yomwe ili pa tsamba 10 ndi 11, ndipo limbikitsani onse kuti akonzekeretse mitima yawo. (Eza 7:10) Fotokozani zimene mpingo wanu wakonza kuti athu adzakwanitse kuonera kapena kupezeka pamwambowu.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 14 ndime 10-17, mawu akumapeto 30
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 15 ndi Pemphero