Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mungatani Kuti Mukhale Bwenzi Labwino?

Kodi Mungatani Kuti Mukhale Bwenzi Labwino?

Muzitonthoza komanso kulimbikitsa mnzanu amene akuda nkhawa (1Sa 20:1, 2; w19.11 7 ¶18)

Muzichenjeza mnzanu ku zinthu zoopsa (1Sa 20:12, 13; w08 2/15 8 ¶7)

Muzimuikira kumbuyo ena akamamunenera zoipa (1Sa 20:30-32; w09 10/15 19 ¶11)

Anthu a Yehova ali ndi mwayi waukulu wokhala ndi anzawo abwino. Kuti tikhale ndi mabwenzi, tiyenera kukhala aubwenzi. Kodi ndi ndani amene mungakonde kuti akhale mnzanu mumpingo?