Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

March 21-27

1 SAMUELI 16-17

March 21-27

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Yehova Ndiye Mwini Nkhondo”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Sa 16:14, mawu a m’munsi​—Kodi Sauli analandira “mzimu woipa wochokera kwa Yehova” m’njira yotani? (it-2 871-872)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 16:1-13 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuitanira Anthu ku Chikumbutso: (2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene poitanira anthu ku Chikumbutso. (th phunziro 11)

  • Kuitanira Anthu ku Chikumbutso: (3 min.) Itanirani mnzanu wakuntchito, wakusukulu kapena wachibale wanu amene munamulalikirapo m’mbuyomu. (th phunziro 2)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. (th phunziro 4)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. Mudziwitseni za webusaiti yathu. (th phunziro 20)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU