CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Tizidzichepetsa Zinthu Zikatiyendera
Aisiraeli anatamanda Davide (1Sa 18:5-7; w04 4/1 15 ¶4)
Yehova ankathandiza Davide kuti zinthu zimuyendere bwino (1Sa 18:14)
Davide anapitiriza kukhala wodzichepetsa (1Sa 18:22, 23; w18.01 28 ¶6-7)
N’chifukwa chiyani tiyenera kukhalabe odzichepetsa Yehova akamatidalitsa? Kodi n’chiyani chingatithandize kuti tikhalebe odzichepetsa?