Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kudzikuza Kumabweretsa Manyazi

Kudzikuza Kumabweretsa Manyazi

Mfumu Sauli inkamva kuti yapanikizika (1Sa 13:5-7)

Sauli anachita zinthu modzikuza m’malo motsatira malangizo a Yehova modzichepetsa (1Sa 13:8, 9; w00 8/1 13 ¶17)

Yehova anadzudzula Sauli (1Sa 13:13, 14; w07 6/15 27 ¶8)

Munthu amasonyeza kuti ndi wodzikuza akachita zinthu zomwe si udindo wake mopupuluma kapena mopusa. Kudzikuza n’kosiyana ndi kudzichepetsa. Kodi ndi pazochitika ziti pamene munthu angayesedwe kuti achite zinthu modzikuza?