Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

April 10-16

2 Mbiri 8-9

April 10-16

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Mfumukazi Inaona Kuti Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mb 9:19​—Kodi n’kutheka kuti zifaniziro 12 za mikango zomwe zinali pa masitepe okafika kumpando wachifumu wa Solomo zinkaimira chiyani? (it-2 1097)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 8:1-16 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU