Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfumukazi ya ku Sheba yakacheza kwa Mfumu Solomo

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mfumukazi Inaona Kuti Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali

Mfumukazi Inaona Kuti Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali

Mfumukazi ya ku Sheba inayenda ulendo wautali komanso wovuta kuti ikaone Solomo (2Mb 9:1, 2; w99 11/1 20 ¶4; w99 7/1 30 ¶4-5)

Nzeru komanso chuma cha Solomo zinamusowetsa chonena (2Mb 9:3, 4; w99 7/1 30-31; onani chithunzi chapachikuto)

Zimene anaona zinamuchititsa kuti atamande Yehova (2Mb 9:7, 8; it-2 990-991)

Mfumukazi ya ku Sheba inaona kuti nzeru ndi zamtengo wapatali moti inachita zonse zomwe ikanatha kuti ikhale nazo.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndine wofunitsitsa kufunafuna nzeru ngati mmene ndingachitire ndi chuma chobisika?’​—Miy 2:1-6.