Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

April 17-23

2 MBIRI 10-12

April 17-23

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Muzitsatira Malangizo Anzeru”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mb 11:15​—Kodi mawu akuti “ziwanda zooneka ngati mbuzi” angakhale akunena za chiyani? (it-1 966-967)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 10:1-15 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 12)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 6)

  • Nkhani: (5 min.) be 69 ¶4-5​—Mutu: Ophunzira Baibulo Akafunsa Malangizo, Muziwaphunzitsa Mmene Angawapezere. (th phunziro 20)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU