Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzitsatira Malangizo Anzeru

Muzitsatira Malangizo Anzeru

Rehobowamu anafunika kusankha zochita (2Mb 10:1-4; w18.06 13 ¶3)

Rehobowamu anafunsira malangizo (2Mb 10:6-11; w01 9/1 28-29)

Rehobowamu ndi anthu ena anakumana ndi mavuto chifukwa iye sanatsatire malangizo anzeru (2Mb 10:12-16; it-2 768 ¶1)

Chifukwa cha luso komanso msinkhu wawo, Akhristu olimba mwauzimu nthawi zina akhoza kudziwiratu mmene zinthu zingathere.​—Yob 12:12.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndi ndani mumpingo amene angandipatse malangizo abwino?’