April 24-30
2 MBIRI 13-16
Nyimbo Na. 3 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Ndi pa Nthawi Iti Pamene Tiyenera Kudalira Yehova?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mb 15:16—Kodi tingatsanzire bwanji kulimba mtima kwa Asa? (w17.03 19 ¶7)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 14:1-15 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muuzeni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu ndipo musiyireni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 11)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 09 mfundo 7 ndi Zimene Ena Amanena (th phunziro 6)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Zosankha Zomwe Zimasonyeza Kuti Timadalira Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 44 mfundo 1-4 ndi mawu akumapeto 5
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 39 ndi Pemphero