CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Kodi Ndi pa Nthawi Iti Pamene Tiyenera Kudalira Yehova?
Asa anadalira Yehova kuti agonjetse gulu lalikulu la asilikali (2Mb 14:9-12; w21.03 5 ¶12)
Patapita nthawi Asa anadalira Asiriya kuti agonjetse gulu laling’ono la asilikali (2Mb 16:1-3; w21.03 5 ¶13)
Yehova sanasangalale ndi Asa chifukwa anasiya kumudalira (2Mb 16:7-9)
Tikhoza kudalira Yehova tikamapanga zosankha zikuluzikulu zimene zingasinthe moyo wathu, koma bwanji panthawi zina? M’pofunika kuti tizikumbukira Yehova m’njira zathu zonse.—Miy 3:5, 6; w21.03 6 ¶14.