Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

March 13-19

1 MBIRI 27-29

March 13-19

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Wobwereza: Yesu​—Mt 20:28. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa chiyani Yesu anafa?, kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 9)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. Yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 6)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU