Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Malangizo Achikondi a Bambo Opita kwa Mwana Wake

Malangizo Achikondi a Bambo Opita kwa Mwana Wake

Um’dziwe bwino Yehova (1Mb 28:9; w05 2/15 19 ¶9)

Um’tumikire Yehova ndi mtima wathunthu (1Mb 28:9; w12 4/15 16 ¶13)

Uzidalira Yehova ndipo usachite mantha (1Mb 28:20; w17.09 32 ¶20-21)

Mfumu Davide yemwe panthawiyi anali wachikulire, anapereka malangizo amenewa kwa mwana wake Solomo amene anali wosadziwa zambiri pamene ankafuna kuyamba kugwira ntchito yofunika kwambiri yomanga kachisi. N’chifukwa chiyani malangizo amenewa ali ofunika kwambiri kwa aliyense, koma makamaka achinyamata Achikhristu?