CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Mfumu Solomo Inasankha Zinthu Mopanda Nzeru
[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Mbiri.]
Solomo anasonkhanitsa mahatchi ndi magaleta ochokera ku Iguputo (De 17:15, 16; 2Mb 1:14, 17)
Pankafunika anthu komanso mizinda yambiri kuti asamalire mahatchi komanso magaletawa (2Mb 1:14; it-1 174 ¶5; 427)
Ngakhale kuti anthu anakhala moyo wosangalala mu zaka zoyambirira za ulamuliro wa Solomo, iwo anagalukira mu ufumu wa Rehobowamu chifukwa iye anawonjezera goli lolemera lomwe anali nalo. (2Mb 10:3, 4, 14, 16) Nthawi zonse zomwe timasankha zimakhala ndi zotsatirapo zake.—Aga 6:7.