March 27–April 2
2 MBIRI 5-7
Nyimbo Na. 129 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mtima Wanga Udzakhala Pamenepa Nthawi Zonse”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mb 6:29, 30—Kodi mawu otchulidwa mu pemphero la Solomowa angatilimbikitse bwanji? (w10 12/1 11 ¶7)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 6:28-42 (th phunziro 11)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kuitanira Anthu ku Chikumbutso: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha zimene tinganene. Ngati mwininyumba wasonyeza chidwi yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Tizikumbukira Imfa ya Yesu, kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Pambuyo pa nkhani ya Chikumbutso, yambani kukambirana ndi munthu amene munamuitana ndipo muyankhe funso limene wafunsa lokhudza mwambowu. (th phunziro 17)
Nkhani: (5 min.) w93 2/1 31—Mutu: Kodi Tingatani Ngati Sitingakwanitse Kupezeka pa Chikumbutso pa Zifukwa Zina? (th phunziro 18)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Uteteze Mtima Wako”: (10 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Zofunika Pampingo: (5 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 41 mfundo 5, zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 34 ndi Pemphero