Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

“Uteteze Mtima Wako”

“Uteteze Mtima Wako”

Yehova anauzira Solomo kulemba kuti: “Uteteze mtima wako kuposa zonse zimene ziyenera kutetezedwa.” (Miy 4:23) Koma n’zomvetsa chisoni kuti Aisiraeli omwe anali anthu a Mulungu anasiya kutumikira Yehova “ndi mtima wawo wonse.” (2Mb 6:14) Ngakhale Mfumu Solomo inalola kuti akazi omwe sankalambira Yehova apotoze mtima wake n’kuyamba kulambira milungu ina. (1Mf 11:4) Kodi tingateteze bwanji mtima wathu? Nkhaniyi ili mu Nsanja ya Olonda yophunzira ya January 2019, tsamba 14-19.

ONERANI VIDIYO YAKUTI ZIMENE TINAPHUNZIRA MU NSANJA YA OLONDA​—KODI TINGATETEZE BWANJI MTIMA WATHU?, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

Kodi n’chiyani chimene chikanafooketsa chikhulupiriro cha Akhristuwa, nanga nkhani yophunzirayi inawathandiza bwanji kuteteza mtima wawo?

  • Brent ndi Lauren

  • Umjay

  • Happy Layou

Kodi nkhani yophunzira imeneyi inakuthandizani bwanji?