Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kulambira kwa Pakachisi Kunali kwa Dongosolo

Kulambira kwa Pakachisi Kunali kwa Dongosolo

Mfumu Davide inakonza zoti Alevi ndi ansembe azitumikira pakachisi (1Mb 23:6, 27, 28; 24:1, 3; it-2 241, 686)

Akatswiri oimba komanso ophunzira kuimba anapatsidwa utumiki wokonza nyimbo (1Mb 25:1, 8; it-2 451-452)

Alevi anapatsidwa utumiki woyang’anira chuma, ena anali alonda a pachipata komanso ena anapatsidwa maudindo osiyanasiyana (1Mb 26:16-20; it-1 898)

Timalambira Yehova mwadongosolo chifukwa iye ndi Mulungu wadongosolo.​—1Ak 14:33.

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi mpingo wa Chikhristu masiku ano umasonyeza bwanji kuti umalambira Yehova mwadongosolo?