March 10-16
MIYAMBO 4
Nyimbo Na. 36 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. “Muziteteza Mtima Wanu”
(10 min.)
Mawu akuti “mtima” amatanthauza munthu wamkati (Sl 51:6; w19.01 15 ¶4)
Chinthu chofunika kwambiri pa moyo wathu chiyenera kukhala kuteteza mtima wathu (Miy 4:23a; w19.01 17 ¶10-11; 18 ¶14; onani chithunzi)
Kuti tikhalebe ndi moyo zimadalira kuti mtima wathu wophiphiritsa uli bwanji (Miy 4:23b; w12 5/1 32 ¶2)
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Miy 4:18—Kodi vesili likutithandiza bwanji kumvetsa mmene Mkhristu amasinthira zinthu pa moyo wake n’cholinga choti akhale pa ubwenzi ndi Yehova? (w21.08 8 ¶4)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Miy 4:1-18 (th phunziro 12)
4. Ulendo Woyamba
(3 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Munthu wasonyeza chidwi mutamuitanira ku Chikumbutso. (lmd phunziro 1 mfundo 5)
5. Ulendo Woyamba
(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Itanirani mnzanu ku Chikumbutso. (lmd phunziro 2 mfundo 3)
6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupirira
(5 min.) Chitsanzo. ijwfq nkhani na. 19—Mutu: N’chifukwa Chiyani Simukondwerera Isitala? (lmd phunziro 3 mfundo 4)
Nyimbo Na. 16
7. Vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya March
(10 min.) Onerani VIDIYOYI.
8. Ntchito Yoitanira Anthu ku Chikumbutso Iyamba Loweruka pa 15 March
(5 min.) Nkhani yokambidwa ndi woyang’anira utumiki. Fotokozani zimene mpingo wanu wakonza zokhudza kugwira ntchitoyi, kumvetsera nkhani yapadera komanso mwambo wa Chikumbutso. Limbikitsani onse kuti ayesetse kuchita zambiri mu utumiki m’miyezi ya March ndi April.
9. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) bt mutu 23 ¶16-19, bokosi patsamba 188