NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU May 2018
Zimene Tinganene
Zimene tinganene zokhudza tsogolo la anthu komanso dziko lapansi.
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Nyamula Mtengo Wako Wozunzikirapo, ndi Kunditsatira Mosalekeza
N’chifukwa chiyani sitiyenera kusiya kupemphera, kuphunzira Baibulo, kulalikira komanso kusonkhana?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Muzithandiza Ana Anu Kuti Akhale Otsatira a Khristu
Kodi makolo angatani kuti athandize ana awo kuti adzipereke kwa Yehova komanso kubatizidwa?
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Masomphenya Olimbitsa Chikhulupiriro
Kodi masomphenyawa anathandiza bwanji mtumwi Petulo? Kodi kukwaniritsidwa kwa maulosi a m’Baibulo kungatithandize bwanji masiku ano?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Chimene Mulungu Wachimanga Pamodzi . . . ”
Mabanja achikhristu amalemekeza zimene analonjeza patsiku la ukwati wawo. Iwo amayesetsa kuthana ndi mavuto potsatira mfundo za m’Baibulo.
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Anaponya Zochuluka Kuposa Onse
Kodi tikuphunzira chiyani mu nkhani ya mayi wamasiye yemwe anapereka timakobidi tiwiri tating’ono kwambiri?
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Pewani Msampha Woopa Anthu
N’chifukwa chiyani atumwi anakodwa mumsampha woopa anthu? Yesu ataukitsidwa, n’chiyani chinathandiza atumwi kuti asamaope anthu n’kumalalikirabe ngakhale kuti ankatsutsidwa?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Yehova Akuthandiza Kuti Ukhale Wolimba Mtima
Kodi nthawi zina mumachita mantha kulalikira kapena kuwauza anthu ena kuti ndinu wa Mboni za Yehova? Ngati ndi choncho, kodi n’chiyani chingakuthandizeni kuti ‘muzilimba mtima’ kuuza ena za Yehova?