May 14-20
Maliko 9-10
Nyimbo Na. 22 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Masomphenya Olimbitsa Chikhulupiriro”: (10 min.)
Maliko 9:1—Yesu analonjeza atumwi ake ena kuti adzaona ulemerero umene adzakhale nawo mu Ufumu wake (w05 1/15 12 ¶9-10)
Maliko 9:2-6—Pamene Yesu anasandulika, Petulo, Yakobo ndi Yohane anaona Yesu akuyankhulana ndi “Eliya” komanso “Mose” (w05 1/15 12 ¶11)
Maliko 9:7—Yehova anatsimikizira anthuwa ndi mawu ake kuti Yesu ndi Mwana wake (“Mawu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 9:7, nwtsty)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Maliko 10:6-9—Kodi ndi mfundo iti yokhudza ukwati yomwe Yesu anaitchula palembali? (w08 2/15 30 ¶8)
Maliko 10:17, 18—N’chifukwa chiyani Yesu anakana, munthu wina atamutchula kuti “Mphunzitsi Wabwino”? (“Mphunzitsi Wabwino” “Palibe wabwino koma Mulungu yekha” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 10:17, 18, nwtsty)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliko 9:1-13
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w04 5/15 30-31—Mutu: Kodi Mawu a Yesu Opezeka pa Maliko 10:25 Amatanthauza Chiyani?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Chimene Mulungu Wachimanga Pamodzi . . . ”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Chikondi ndi Ulemu Zimachititsa Banja Kukhala Logwirizana.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 18 ¶1-8 komanso tsamba 192-193
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 66 ndi Pemphero