May 21-27
MALIKO 11-12
Nyimbo Na. 34 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Anaponya Zochuluka Kuposa Onse”: (10 min.)
Maliko 12:41, 42—Yesu anaona mkazi wamasiye akuponya makobidi awiri aang’ono moponyamo zopereka (“moponyamo zopereka” “timakobidi tiwiri tating’ono” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 12:41, 42, nwtsty)
Maliko 12:43—Yesu anayamikira kwambiri zimene mayiyu anachita ndipo anafotokozera ophunzira ake (w97 10/15 16-17 ¶16-17)
Maliko 12:44—Zimene mayiyu anapereka zinali zamtengo wapatali kwa Yehova (w97 10/15 17 ¶17; w87 12/1 30 ¶1; cl 185 ¶15)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Maliko 11:17—N’chifukwa chiyani Yesu ananena kuti kachisi ndi “nyumba yopemphereramo mitundu yonse”? (“nyumba yopemphereramo mitundu yonse” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 11:17, nwtsty)
Maliko 11:27, 28—Kodi “zinthu” zomwe anthu otsutsa Yesuwa ankanena ndi ziti? (jy 244 ¶7)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliko 12:13-27
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene. Munthuyo wakufotokozerani kuti wachibale wake wamwalira posachedwapa.
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Kukhulupirira Yehova Kumathandiza Kuti Zinthu Zitheke: (15 min.) Onerani vidiyoyi.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 18 ¶9-20 komanso tsamba 199, 200-201
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 98 ndi Pemphero