Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

May 28–June 3

MALIKO 13-14

May 28–June 3

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Pewani Msampha Woopa Anthu”: (10 min.)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Maliko 14:51, 52​—Kodi mnyamata amene anathawa ali malisecheyu ayenera kuti anali ndani? (w08 2/15 30 ¶6)

    • Maliko 14:60-62​—Kodi n’kutheka kuti Yesu anasankha kuyankha funso la mkulu wa ansembe chifukwa chiyani? (jy 287 ¶4)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliko 14:43-59

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene. Muitanireni kumisonkhano yathu.

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba limene mukufuna kugwiritsira ntchito. M’patseni buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 181-182 ¶17-18

MOYO WATHU WACHIKHRISTU