June 14-20
DEUTERONOMO 5-6
Nyimbo Na. 134 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Phunzitsani Ana Anu Kuti Azikonda Yehova”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
De 5:21—Kodi lamulo loletsa kusirira kwa nsanje limatiphunzitsa chiyani? (w19.02 22 ¶11)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 5:1-21 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (th phunziro 9)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Sinthani ulaliki wanu kuti ugwirizane ndi nkhani imene mwininyumba watchula, ndipo werengani lemba logwirizana ndi nkhaniyo. (th phunziro 12)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) fg phunziro 9 ¶6-7 (th phunziro 8)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 105
“Muzisonyeza Chikondi M’banja”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzisonyeza Chikondi Chosatha M’banja.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 138
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 22 ndi Pemphero