Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Phunzitsani Ana Anu Kuti Azikonda Yehova

Phunzitsani Ana Anu Kuti Azikonda Yehova

Makolo ayenera kumakonda kwambiri Yehova (De 6:5; w05 6/15 20 ¶11)

Makolo ayenera kupereka chitsanzo chabwino kwa ana awo (De 6:6; w07 5/15 15-16)

Makolo ayenera kumaphunzitsa ana awo zokhudza Yehova nthawi zonse (De 6:7; w05 6/15 21 ¶14)

Kuwonjezera pa kulambira kwa pabanja, kodi ndi pa nthawi zinanso ziti pamene mungaphunzitse ana anu kuti azikonda Yehova komanso mfundo zake?