June 28–July 4
DEUTERONOMO 9-10
Nyimbo Na. 49 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Yehova Mulungu Wanu Akufuna Kuti Muzichita Chiyani?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
De 9:1-3—Ngakhale kuti ana a Anaki anali “amphamvu ndi aatali,” n’chifukwa chiyani Aisiraeli sankafunika kuwaopa? (it-1 103)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 10:1-22 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? ndipo kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 9)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) fg phunziro 12 ¶4-5 (th phunziro 18)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 135
Kodi Mumakonda Kusewera Magemu a Pakompyuta?: (7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi magemu a pakompyuta angakhale ndi mavuto otani? Kodi ndi zinthu ziti zomwe n’zofunika kwambiri kuposa magemu a pakompyuta? (Aef 5:15, 16) Kodi magemu amene mumakonda kusewera amasonyeza kuti ndinu munthu wotani? Kodi mungatani kuti magemu a pakompyuta asamakulamulireni?
“Muzisankha Zinthu Mwanzeru pa Nkhani ya Mowa”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Ganizirani Zimene Zingachitike Ngati Mutamwa Mowa.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs Kalata Yochokera ku Bungwe Lolamulira, mutu 1 ndime 1-6, Mawu Akumapeto 1
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 105 ndi Pemphero