June 7-13
DEUTERONOMO 3-4
Nyimbo Na. 98 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Malamulo a Yehova Amasonyeza Kuti Ndi Wanzeru Komanso Wachilungamo”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
De 4:23—Kodi n’chiyani chimene Aisiraeli analetsedwa kuchita palembali? (w04 9/15 25 ¶7)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 3:1-13 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
“Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki—Muziphunzitsa Ndi Mtima Wonse”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa—Muziphunzitsa ndi Mtima Wonse.
Phunziro la Baibulo: (5 min.) fg phunziro 5 ¶1-2 (th phunziro 11)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 68
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 137
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 69 ndi Pemphero