CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Malamulo a Yehova Amasonyeza Kuti Ndi Wanzeru Komanso Wachilungamo
Timasonyeza kuti ndife anzeru komanso ozindikira tikamamvera malamulo a Mulungu (De 4:6; it-2 1140 ¶5)
Anthu omwe amaona zochita zathu amazindikira kuti malamulo a Mulungu amatithandiza kukhala anzeru (De 4:6; w99 11/1 20 ¶6-7)
Anthu a Yehova amakhala moyo wosangalala kuposa anthu am’dzikoli (De 4:7, 8; w07 8/1 29 ¶13)
Anthu ambiri amabwera m’gulu la Yehova akaona makhalidwe abwino a anthu omwe amatsatira malamulo komanso mfundo za Mulungu pa moyo wawo.
Kodi mwapeza madalitso otani chifukwa chotsatira malangizo anzeru ochokera kwa Yehova?