May 17-23
NUMERI 32-33
Nyimbo Na. 142 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mukathamangitse Anthu Onse a M’dzikolo”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Nu 33:54—Kodi malo ankagawidwa bwanji ku mafuko a Aisiraeli? (it-1 359 ¶2)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 32:28-42 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
“Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki—Muzigwiritsa Ntchito Mafanizo”: (10 min.) Nkhani Yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa—Muzigwiritsa Ntchito Mafanizo.
Nkhani: (5 min.) w09 10/1 30, bokosi—Mutu: N’chifukwa Chiyani Yehova Ankadalitsa Nkhondo Zimene Aisiraeli Akale Ankamenya? (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 58
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 134
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero