Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Thawirani kwa Yehova

Thawirani kwa Yehova

Mu Isiraeli munali mizinda 6 yoti amene wapha munthu mwangozi azithawirako (Nu 35:15; w17.11 9 ¶4)

Akulu a mu Isiraeli ankaweruza mlandu uliwonse (Nu 35:24; w17.11 9 ¶6)

Mizinda yothawirako inali malo achitetezo (Nu 35:25; w17.11 11 ¶13)

Mofanana ndi munthu yemwe wapha mnzake mwangozi amene ankafunika kusiya moyo umene anazolowera kuti akhale ndi mwayi wotetezedwa ndi mizinda yothawirako, ifenso timafunika kusiya zinthu zina kuti Yehova atichitire chifundo n’kutikhululukira.