Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

May 3-9

NUMERI 27-29

May 3-9
  • Nyimbo Na. 106 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 82

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Uzikonda Mnzako: (6 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako ngati n’zotheka, funsani ana omwe munawasankhiratu mafunso awa: N’chifukwa chiyani ana ena sankafuna kuchita zinthu ndi Priya kusukulu? Kodi Sofiya anasonyeza bwanji chikondi kwa Priya? Kodi mungasonyeze bwanji chikondi kwa anthu omwe ndi osiyana ndi inu?

  • Kodi Mnzako Weniweni Ungamudziwe Bwanji?: (9 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yamakatuniyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi muyenera kuyang’ana zinthu ziti mukamasankha anzanu? Kodi anzanu abwino mungawapeze kuti? Kodi mungatani kuti ubwenzi wanu uziyenda bwino?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 132 ndi bokosi lakuti “Mpachikeni”

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 20 ndi Pemphero