Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Mukuweruzira Mulungu”

“Mukuweruzira Mulungu”

[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Deuteronomo]

Akulu ayenera ‘kumaweruza mwachilungamo’ (De 1:16; w96 3/15 23 ¶1)

Akulu sayenera ‘kukondera poweruza’ (De 1:17; w02 8/1 10 ¶4)

Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira kuti tili ndi akulu?​—Ahe 13:17; Yak 5:13-15