June 13-19
2 SAMUELI 11-12
Nyimbo Na. 121 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Musalole Kuti Zilakolako Zoipa Zizikulamulirani”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Sa 12:13—Kodi Yehova sanaphe Davide ndi Batiseba pa zifukwa ziti? (it-1 590 ¶1)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 11:1-15 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 11)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale ndipo yambitsani phunziro la Baibulo mu phunziro 01. (th phunziro 13)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 05 mfundo 5 (th phunziro 15)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muzidziletsa”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Musawononge Moyo Wanu Chifukwa cha Kusuta.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 08
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 28 ndi Pemphero