June 20-26
2 SAMUELI 13-14
Nyimbo Na. 127 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kudzikonda kwa Aminoni Kunabweretsa Mavuto”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Sa 14:25, 26—Kodi chitsanzo cha Abisalomu chimatiphunzitsa chiyani pa nkhani ya kukongola? (g05 1/8 24-25)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 14:8-20 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Gawirani magazini yomwe ili ndi nkhani imene mwininyumba anatchula. (th phunziro 12)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muitanireni kumisonkhano yathu. (th phunziro 18)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 05 mfundo 6 komanso Zimene Ena Amanena (th phunziro 18)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muzigwiritsa Ntchito Buku Lakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale Polimbitsa Chikhulupiriro Chanu mwa Yehova Ndi Yesu”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzilimbitsa Chikhulupiriro Chanu mwa Yehova Pogwiritsa Ntchito Buku Lakuti “Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale” komanso yakuti Muzilimbitsa Chikhulupiriro Chanu mwa Yesu Pogwiritsa Ntchito Buku Lakuti “Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale.”
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 09
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 47 ndi Pemphero