Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kudzikonda kwa Aminoni Kunabweretsa Mavuto

Kudzikonda kwa Aminoni Kunabweretsa Mavuto

Aminoni anatengeka ndi Tamara (2Sa 13:1, 2; it-1 32)

Aminoni anagwiririra Tamara (2Sa 13:10-15; w17.09 5 ¶11)

Abisalomu anachititsa kuti Aminoni aphedwe (2Sa 13:28, 29; it-1 33 ¶1)

Kodi amene ali pachibwenzi angapewe bwanji mavuto? Angasonyeze kuti ndi anzeru komanso odziletsa akamapewa malo kapena zochitika zimene zingawapangitse kuti achite zolakwika.