June 27–July 3
2 SAMUELI 15-17
Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Abisalomu Anaukira Chifukwa cha Kunyada”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Sa 16:4—Kodi tikuphunzirapo chiyani pa mmene Davide anachitira zinthu mopupuluma? (w18.08 6 ¶11)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 17:17-29 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 7)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (th phunziro 2)
Nkhani: (5 min.) w09 5/15 27-28—Mutu: Muzichita Zinthu Mwakhama Ngati Itai Mukakhala mu Utumiki.—2Sa 15:19-22. (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (5 min.)
“Chikondi . . . Sichidzikuza”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzikumbukira Zimene Chikondi Chimachita Komanso Zimene Sichichita—Sichidzikuza.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 10
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 87 ndi Pemphero