Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Abisalomu Anaukira Chifukwa cha Kunyada

Abisalomu Anaukira Chifukwa cha Kunyada

Abisalomu anadzifunira yekha ulemerero (2Sa 15:1; it-1 860)

Abisalomu anakopa mitima ya anthu (2Sa 15:2-6; w12 7/15 13 ¶5)

Abisalomu ankafuna kulanda ufumu wa bambo ake (2Sa 15:10-12; it-1 1083-1084)

Tisalole kuti kulakalaka kwambiri zinthu kuzilamulira mtima wathu. Koma nthawi ndi nthawi tizionanso zimene timalakalaka. M’malo momangofuna kugometsa anthu ena, tiziyesetsa kuganiziranso zofuna zawo.​—Afi 2:3, 4.