May 16-22
2 Samueli 1-3
Nyimbo Na. 103 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Tikuphunzira Chiyani Kuchokera pa Nyimbo Yotchedwa ‘Uta’?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Sa 1:26—N’chifukwa chiyani Davide anatchula Yonatani kuti “m’bale wanga”? (it-1 369 ¶2)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 3:1-16 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mufotokozereni zokhudza phunziro la Baibulo la ulele, kenako m’patseni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 20)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 04 mfundo 5 komanso Zimene Ena Amanena (th phunziro 19)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Chikondi . . . Sichikondwera ndi Zosalungama”: (7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzikumbukira Zimene Chikondi Chimachita Komanso Zimene Sichichita—Sichikondwera ndi Zosalungama.
“Chikondi . . . Chimayembekezera Zinthu Zonse”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzikumbukira Zimene Chikondi Chimachita Komanso Zimene Sichichita—Chimayembekezera Zinthu Zonse.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 04
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 2 ndi Pemphero