Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Tikuphunzira Chiyani Kuchokera pa Nyimbo Yotchedwa “Uta”?

Kodi Tikuphunzira Chiyani Kuchokera pa Nyimbo Yotchedwa “Uta”?

[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Samueli.]

Tizilemekeza anthu audindo (2Sa 1:17, 18, 23, 24; w00 6/15 13 ¶9)

Tizikhala okhulupirika kwa anzathu (2Sa 1:25, 26; w12 4/15 10 ¶8)

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimalemekeza akulu mumpingo? Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndine wokhulupirika kwa Akhristu anzanga?’