Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

May 2-8

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 129

  • Anakhalabe Olimba Pozunzidwa: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi tikuphunzira chiyani pa chitsanzo cha abale athu a ku Germany mu ulamuliro wa Nazi? Kodi tikuphunzira chiyani pa chitsanzo cha abale athu a ku Russia komanso dziko lomwe kale linali Soviet Union?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 02

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 94 ndi Pemphero