Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mmene Davide Ankamenyera Nkhondo

Mmene Davide Ankamenyera Nkhondo

Davide ankafuna kuthawa Sauli (1Sa 27:5-7; it-1 41)

Davide anateteza malire a Yuda (1Sa 27:8, 9; w21.03 4 ¶8)

Davide sanauze Akisi zonse zimene ankachita (1Sa 27:10-12; it-2 245 ¶6)

Masiku ano akuluakulu a boma akhoza kuletsa ntchito yathu ya Ufumu komanso akhoza kutifunsa zokhudza abale athu. Pa nthawi ngati imeneyi ndi bwino kukhala chete kuti tisaike abale athu pangozi.—Miy 10:19; 11:12; Mla 3:7.