May 23-29
2 SAMUELI 4-6
Nyimbo Na. 135 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzikhala Ndi Mantha Oyenera Poopa Kukhumudwitsa Yehova”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Sa 6:8, 9—Kodi tikuphunzira chiyani pa zimene Davide anachita Yehova atakwiya? (w96 4/1 29 ¶1)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4min.) 2Sa 4:1-12 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 12)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? (th phunziro 9)
Nkhani: (5 min.) w05 10/1 23-24 ¶14-15—Mutu: “Opani Mulungu ndi Kumupatsa Ulemerero.”—Chv 14:7. (th phunziro 19)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kodi Mwakonzeka Kukumana ndi Zachiwawa?”: (15 min.) Nkhani yokambirana yokambidwa ndi mkulu. Onerani vidiyo yakuti Kodi Mwakonzeka Kukumana ndi Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi?. Tchulaninso zilengezo zochokera ku ofesi ya nthambi kapena ku bungwe la akulu ngati zilipo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 05
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 96 ndi Pemphero