Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzikhala Ndi Mantha Oyenera Poopa Kukhumudwitsa Yehova

Muzikhala Ndi Mantha Oyenera Poopa Kukhumudwitsa Yehova

Zolinga zabwino sizisintha zimene Mulungu amafuna (2Sa 6:3-5; w05 5/15 17 ¶7)

Uza sanamvere Chilamulo cha Mulungu (2Sa 6:6; w05 2/1 27 ¶20)

Yehova analanga Uza chifukwa choti sanamulemekeze (2Sa 6:7; w05 2/1 27 ¶21)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimaopa kukhumudwitsa Yehova pa moyo wanga?’​—Miy 3:7