May 30–June 5
2 SAMUELI 7-8
Nyimbo Na. 22 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Anachita Pangano ndi Davide”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Sa 8:2—Kodi mmene Davide anagonjetsera Amowabu zinakwaniritsa bwanji ulosi? (it-2 206 ¶2)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 7:1-17 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba, kenako mugwirizanitse ndi zimene zikuchitika m’dera lanu. Mugawireni magazini yomwe ili ndi nkhani imene anatchula. (th phunziro 13)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza, kenako mugwirizanitse ndi zimene zikuchitika m’dera lanu. Mufotokozereni zokhudza phunziro la Baibulo la ulele, ndipo m’patseni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 18)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 04 zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga (th phunziro 8)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (10 min.)
“Muzigwiritsa Ntchito Zimene Zikuchitika M’dera Lanu Mukakhala mu Utumiki”: (5 min.) Nkhani yokambirana.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 06
Mawu Omaliza (3 min.)