Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

May 9-15

1 SAMUELI 30-31

May 9-15

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 43

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Muzipemphera Nthawi Iliyonse: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako ngati n’zotheka, funsani ana omwe munawasankhiratu mafunso awa: N’chifukwa chiyani tiyenera kupemphera kwa Yehova? Kodi ndi pa nthawi ziti pamene tiyenera kupemphera? Kodi ndi zinthu ziti zimene mungatchule m’pemphero?

  • Zofunika Pampingo: (10 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 03

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 95 ndi Pemphero