Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Dzilimbitseni mwa Yehova Mulungu Wanu

Dzilimbitseni mwa Yehova Mulungu Wanu

Aamaleki anawotcha mzinda wa Zikilaga ndi kugwira anthu ake (1Sa 30:1, 2)

Davide ndi amuna amene anali nawo anasweka mtima kwambiri (1Sa 30:3-5; w06 8/1 28 ¶12)

Davide anapeza mphamvu kwa Yehova (1Sa 30:6; w12 4/15 30 ¶14)

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi ndikapanikizika ndimapeza mphamvu kuchokera kwa ndani?