Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

Zimene Tinganene

Zimene Tinganene

Ulendo Woyamba *

Funso: Kodi timadziwa bwanji kuti mavuto omwe timakumana nawo si chilango chochokera kwa Mulungu?

Lemba: Yak 1:13

Funso la Ulendo Wotsatira: N’chifukwa chiyani timavutika?

Ulendo Wobwereza *

Funso: N’chifukwa chiyani timavutika?

Lemba: 1Yo 5:19

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Mulungu amamva bwanji akamationa tikuvutika?

^ ^ Mukhoza kusintha mafunsowa komanso zimene zikuchitika kuti zigwirizane ndi mmene zinthu zilili kwanuko.